Judges 3:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamwalira Ehudi, padabwera Samigara, mwana wa Anati, amene adapha Afilisti 600 ndi ndodo yomenyera ng'ombe. Motero iyeyunso adapulumutsa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atapita iye kunali Samigara, mwana wa Anati amene anakantha Afilisti mazana asanu ndi limodzi ndi mtoso wa ng'ombe; nayenso anapulumutsa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ehudi atamwalira, panabwera Samugara mwana wa Anati. Iye anapha Afilisti 600 ndi ndodo yomenyera ngʼombe. Nayenso anapulumutsa Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atapita iye kunali Samagara, mwana wa Anati amene anakantha Afilisti mazana asanu ndi limodzi ndi mtoso wa ng'ombe; nayenso anapulumutsa Israyeli.