Judges 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraelewo adayamba kukwatirana ndi anthu a mitundu imeneyo, ndiponso kukwatitsa ana ao kwa amuna a mitundu inayo. Kenaka adayamba kupembedza milungu yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakwatira ana akazi a iwowa, napereka ana ao akazi kwa ana amuna a iwowa natumikira milungu yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Aisraeli aja amalola ana awo aamuna ndi aakazi kuti azikwatira ndi kukwatiwa ndi anthu amitundu ina. Kenaka anayamba kupembedza milungu yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nakwatira ana akazi a iwowa, napereka ana ao akazi kwa ana amuna a iwowa natumikira milungu yao.