Judges 3:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adachita zinthu zoipira Chauta. Adaiŵala Chauta, Mulungu wao, namatumikira mafano a Abaala ndi Asitaroti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele anachita choipa pamaso pa Yehova, naiwala Yehova Mulungu wao, natumikira Abaala ndi zifanizo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli anachita zinthu zoyipira Yehova. Iwowa anayiwala Yehova Mulungu wawo ndi kumatumikira Abaala ndi Asera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli anacita coipa pamaso pa Yehova, naiwala Yehova Mulungu wao, natumikira Abaala ndi zifanizo.