Judges 4:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Baraki adaitana mafuko a Zebuloni ndi a Nafutali kuti abwere ku Kedesi. Anthu amene adamtsata analipo 10,000, ndipo Debora adapita nawo limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Baraki anaitana Zebuloni ndi Nafutali asonkhane ku Kedesi; iye nakwera ndi anthu zikwi khumi akumtsata; Deboranso anakwera kunka naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Baraki anayitana mafuko a Zebuloni ndi Nafutali kuti abwere ku Kedesi. Anthu 10,000 anamutsatira, ndipo Debora anapita naye pamodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Baraki anaitana Zebuloni ndi Nafitali asonkhane ku Kedesi; iye nakwera ndi anthu zikwi khumi akumtsata; Deboranso anakwera kumka naye.