Judges 4:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo Mkeni wina, dzina lake Hebere, anali atadzipatula mwa Akeni anzake, zidzukulu za Hobabu, mlamu wa Mose, ndipo adakamanga hema lake kutali, pafupi ndi mtengo wa thundu ku Zananimu, pafupi ndi Kedesi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Hebere Mkeni anadzisiyanitsa ndi Akeni, ndi ana a Hobabu mlamu wake wa Mose, namanga mahema ake mpaka thundu wa m'Zaananimu, ndiwo wa ku Kedesi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi imeneyo nʼkuti Mkeni wina dzina lake Heberi atalekana ndi Akeni anzake, zidzukulu za Hobabu, mlamu wa Mose, nakamanga tenti yake pafupi ndi mtengo wa thundu ku Zananimu pafupi ndi Kedesi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Heberi Mkeni anadzisiyanitsa ndi Akeni, ndi ana a Hobabu mlamu wace wa Mose, namanga mahema ace mpaka thundu wa m'Zaananimu, ndiwo wa ku Kedesi.