Judges 4:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamene Sisera adamva kuti Baraki, mwana wa Abinowamu, wapita ku phiri la Tabori,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauza Sisera kuti Baraki mwana wa Abinowamu wakwera kuphiri la Tabori.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Sisera anamva kuti Baraki mwana wa Abinoamu wapita ku phiri la Tabori,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauza Sisera kuti Baraki mwana wa Abinoamu wakwera ku phiri la Tabori.