Judges 4:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adauza mkazi uja kuti, “Mukaime pakhomo pa hema, ndipo munthu aliyense akabwera ndi kukufunsani kuti, ‘Kodi muli munthu m'menemo?’ Mumuuze kuti, Ai, mulibe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sisera ananena naye, Taima pakhomo pa hema, ndipo kudzali, akadza munthu, akakufunsa akati, Pali munthu pano kodi? Uziti, Palibe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anawuza mkaziyo kuti, “Muyime pa khomo la tentili, ndipo munthu wina akabwera kudzakufunsani kuti, ‘Kodi kwafika munthu wina kuno?’ Inu muyankha kuti, ‘Ayi.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Sisera ananena naye, Taima pakhomo pa hema, ndipo kudzali, akadza munthu, akakufunsa akati, Pali munthu pano kodi? Uziti, Palibe.