Judges 4:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Aisraele adapanikizabe Yabini, mfumu ya ku Kanani, mpaka kumuwonongeratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo dzanja la ana a Israele linamkabe ndi kulimbika pa Yabini mfumu ya Kanani mpaka adamuononga Yabini mfumu ya Kanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Aisraeli anapanikizabe Yabini, mfumu ya Akanaani, mpaka kumuwonongeratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dzanja la ana a Israyeli linamkabe ndi kulimbika pa Yabini mfumu ya Kanani mpaka adamuononga Yabini mfumu ya Kanani.