Judges 4:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye ankakhala patsinde pa mtengo wa mgwalangwa wa Debora, pakati pa Rama ndi Betele, m'dziko lamapiri la Efuremu, ndipo Aisraele ankabwera kwa iye kuti aŵaweruze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakhala patsinde pa mgwalangwa wa Debora pakati pa Rama ndi Betele ku mapiri a Efuremu; ndi ana a Israele anakwera kwa iye awaweruze.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ankakhala pansi pa mtengo wa mgwalangwa wa Debora, pakati pa Rama ndi Beteli mʼdziko la ku mapiri la Efereimu, ndipo Aisraeli ankapita kwa iye kuti akaweruze milandu yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakhala patsinde pa mgwalangwa wa Debora pakati pa Rama ndi Beteli ku mapiri a Efraimu; ndi ana a Israyeli anakwera kwa iye awaweruze.