Judges 4:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Debora adati, “Chabwino, ndipita nanu, komatu inu simudzalandirapo ulemu mutapambana, pakuti Chauta adzapereka Sisera m'manja mwa munthu wamkazi.” Tsono Debora adanyamuka kupita ku Kedesi pamodzi ndi Baraki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati iye, Kumuka ndidzamuka nawe, koma ulendo umukawo, sudzachita nao ulemu; pakuti Yehova adzagulitsa Sisera m'dzanja la mkazi. Motero Debora anauka namuka ndi Baraki ku Kedesi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Debora anati, “Chabwino, ine ndipita nawe limodzi. Koma mudziwe kuti inu simudzalandirapo ulemu pa zimene mwachitazi popeza Yehova wapereka Sisera mʼmanja mwa munthu wamkazi.” Choncho Debora ananyamuka kupita ku Kedesi pamodzi ndi Baraki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati iye, Kumuka ndidzamuka nawe, koma ulendo umukawo, sudzacita nao ulemu; pakuti: Yehova adzagulitsa Sisera m'dzanja la mkazi, Motero Debora anauka namuka ndi Baraki ku Kedesi.