Judges 5:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku limenelo la kupambana kwa Debora ndi Baraki, mwana wa Abinowamu, adaimba nyimbo iyi yakuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Debora ndi Baraki mwana wa Abinowamu anaimba tsiku lomwelo ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsiku limenelo Debora ndi Baraki mwana wa Abinoamu anayimba nyimbo iyi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Debora ndi Baraki mwana wa Abinoamu anayimba tsiku lomwelo ndi kuti,