Judges 5:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mafumu adabwera namenya nkhondo, mafumu a ku Kanani adamenya nkhondo ku Taanaki pafupi ndi madzi a ku Megido, koma sadapateko zofunkha zasiliva, kapena china chilichonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anadza mafumu nathira nkhondo; pamenepo anathira nkhondo mafumu a Kanani. M'Taanaki, ku madzi a Megido; osatengako phindu la ndalama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mafumu anabwera, anachita nkhondo; mafumu Akanaani anachita nkhondo ku Tanaki pafupi ndi madzi a ku Megido, koma sanatengeko zofunkha zasiliva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anadza mafumu, nathira nkhondo Pamen'epo anathira nkhondo mafumu a Kanani. M'Taanaki, ku madzi a Megido; Osatengako phindu la ndarama.