Judges 5:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pakuti atsogoleri adatsogoleradi m'dziko la Israele, ndipo anthu adadzipereka okha mwaufulu, tamandani Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lemekezani Yehova pakuti atsogoleri m'Israele anatsogolera, pakuti anthu anadzipereka mwaufulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Popeza kuti atsogoleri anatsogoleradi mʼdziko la Israeli; ndipo anthu anadzipereka okha mwa ufulu, tamandani Yehova:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lemekezani Yehova Pakuti atsogoleri m'Israyeli anatsogolera, Pakuti anthu anadzipereka mwaufulu.