Judges 5:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chigumula cha madzi a mtsinje wa Kisoni chidaŵakokolola onsewo, madzi othamanga, madzi amphamvu a Kisoni. Mtima wanga, limbika, yenda mwamphamvu!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtsinje wa Kisoni unawakokolola, mtsinje uja wakale, mtsinje wa Kisoni. Yenda mwamphamvu, moyo wangawe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsinje wa Kisoni unawakokolola, chigumula cha mtsinje wa Kisoni chinawakokolola. Mtima wanga, yenda mwamphamvu, limbika!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtsinje wa Kisoni unawakokolola, Mtsinje uja wakale, mtsinje wa Kisoni. Yenda mwamphamvu, moyo wangawe.