Judges 5:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mngelo wa Chauta akuti, ‘Utemberere Merozi, utemberere koopsa nzika zake, chifukwa chakuti sizidabwere kudzathandiza Chauta, pakulimbana ndi adani ake amphamvu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutemberere Merozi, ati mthenga wa Yehova, mutemberere chitemberere nzika zake; pakuti sanadzathandize Yehova, kumthandiza Yehova pa achamuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Yehova anati ‘Tembererani Merozi.’ ‘Tembererani nzika zake mwaukali, chifukwa sanabwere kudzathandiza Yehova, kulimbana ndi adani ake amphamvu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutemberere Merozi, ati mthenga wa Yehova, Mutemberere citemberere nzika zace; Pakuti sanadzathandiza Yehova, Kumthandiza Yehova pa acamuna.