Judges 5:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Yaele, mkazi wa Hebere Mkeni, akhale wodala kupambana akazi onse, ndithudi akhale wodala kupambana akazi onse am'dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodalitsika, woposa akazi, akhale Yaele mkazi wa Hebere Mkeni. Akhale wodalitsika woposa akazi a m'hema.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Akhale wodala kupambana akazi onse, Yaeli mkazi wa Heberi Mkeni; inde mwa akazi onse okhala mʼdziko, akhale wodala iyeyu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodalitsika, woposa akazi, akhale Yaeli Mkazi wa Heberi Mkeni. Akhale wodalitsika woposa akazi a m'hema.