Judges 5:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu uja adapempha madzi akumwa, koma Yaele adamupatsa mkaka, adamupatsa chambiko m'chikho chachifumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwamunayo anapempha madzi, anampatsa mkaka, anamtengera mafuta a mkaka m'chotengera cha mfulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu uja anapempha madzi akumwa, koma iye anamupatsa mkaka; anamupatsa chambiko mʼchikho cha wolemekezeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwamunayo anapempha madzi, anampatsa mkaka, Anamtengera mafuta a mkaka m'cotengera ca mfulu.