Judges 5:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sisera adathifuka naagwa; adangoti thasa ku mapazi a Yaele. Adathifukadi nagwera ku mapazi a Yaele. Kumene adaathifukirako, adagwera komweko, naafa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pa mapazi ake anabzong'onyoka, anagwa, anagona; pa mapazi ake anabzong'onyoka, anagwa; pobzong'onyokapo, pamenepo wagwa wafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anathifukira ku mapazi a mkaziyo nagwa, anagwa; iye anagona pamenepo. Anagwera pa mapazi a mkaziyo, iye anagwa; pamene anagwera, pamenepo anaferapo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pa mapazi ace anabzong'onyoka, anagwa, anagona; Pa mapazi ace anabzong'onyoka, anagwa; Pobzong'onyokapo, pamenepo wagwa wafa.