Judges 5:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amai ake anzeru kopambana adamuyankha, mwiniwake yemwenso adadziyankha yekha kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akazi anzake omveka anzeru anamyankha; koma anadziyankhira yekha mau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayi ake anzeru kwambiri anamuyankha, ndithudi, mwiniwake anadziyankha yekha kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akazi anzace omveka anzeru anamyankha; Koma anadziyankhira yekha mau,