Judges 5:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Motero Inu Chauta, adani anu aonongeke! Koma abwenzi anu akhale ngati dzuŵa lotuluka ndi mphamvu zake zonse.” Tsono dziko lidakhala pa mtendere zaka makumi anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adani anu onse, Yehova, atayike momwemo. Koma iwo akukonda Inu akhale ngati dzuwa lotuluka mu mphamvu yake. Ndipo dziko linapumula zaka makumi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Choncho Yehova! adani anu onse awonongeke, koma iwo amene amakukondani inu akhale ngati dzuwa pamene lituluka ndi mphamvu zake.” Ndipo dziko linakhala pa mtendere zaka makumi anayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adani anu onse, Yehova, atayike momwemo. Koma iwo akukonda Inu akhale ngati dzuwa loturuka mu mphamvu yace. Ndipo dziko linapumula zaka makumi anai.