Judges 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pa nthaŵi ya Samigara, mwana wa Anati, pa nthaŵi ya Yaele, m'miseu munali zii, alendo ankangolambalala m'tinjira takumbali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku a Samigara, mwana wa Anati, masiku a Yaele maulendo adalekeka ndi apanjira anayenda mopazapaza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pa nthawi ya Samugara mwana wa Anati, pa nthawi ya Yaeli, misewu inasiyidwa; alendo ankangoyenda mʼtinjira takumbali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku a Samagara, mwana wa Anati, Masiku a Yaeli maulendo adalekeka Ndi apanjira anayenda mopazapaza,