Judges 5:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adaathaŵa ku midzi, midzi idaatha ku Israele, mpaka pamene iwe Debora udafika, udafika ngati mai ku Israele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Milaga idalekeka m'Israele, idalekeka. Mpaka ndinauka ine Debora, ndinauka ine amai wa Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a ku midzi anathawa; mu Israeli munalibe midzi mpaka pamene iwe Debora unafika; unafika ngati mayi ku Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Miraga idalekeka m'Israyeli, idalekeka. Mpaka ndinauka ine Debora, Ndinauka ine amai wa Israyeli.