Judges 5:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga uli ndi atsogoleri a ankhondo a ku Israele, uli ndi anthu amene adadzipereka mwaufulu, kudzipereka mwaufulu pakati pa anzao. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga uvomerezana nao olamulira a m'Israele, amene anadzipereka mwaufulu mwa anthu. Lemekezani Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga uli ndi atsogoleri a Israeli, uli ndi anthu amene anadzipereka okha mwaufulu pakati pa anthu. Tamandani Yehova!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga ubvomerezana nao olamulira a m'Israyeli, Amene anadzipereka mwaufulu mwaanthu. Lemekezani Yehova.