Judges 6:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakuuzani kuti Ine ndine Chauta, Mulungu wanu, musapembedze milungu ya Aamori amene mukukhala m'dziko lao, koma inu simudasamale mau anga.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndinati kwa inu, Ine ndine Yehova Mulungu wanu; musamaopa milungu ya Aamori amene mukhala m'dziko lao; koma simunamvera mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndinakuwuzani kuti, ‘Ine ndine Yehova Mulungu wanu; musapembedze Milungu ya Aamori amene mukukhala mʼdziko lawo.’ Koma inu simunandimvere.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndinati kwa inu, Ine ndine Yehova Mulungu wanu; musamaopa milungu ya Aamori amene mukhala m'dziko lao; koma simunamvera mau anga.