Judges 6:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adamuuza kuti, “Koma Ine ndidzakhala nawe, ndipo udzaŵagonjetsa Amidiyani onse ngati munthu mmodzi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova ananena naye, Popeza Ine ndidzakhala nawe udzakantha Amidiyani ngati munthu mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anamuyankha kuti, “Ine ndidzakhala nawe, ndipo Amidiyaniwo udzawagonjetsa ngati munthu mmodzi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova ananena naye, Popeza Ine ndidzakhala nawe udzakantha Amidyani ngati munthu mmodzi.