Judges 6:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Gideoni adati, “Ngati tsopano mwandikomera mtima, onetseni chizindikiro chosonyeza kuti ndinudi Chauta amene mukulankhula nane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa Iye, Ngati mundikomera mtima mundionetse chizindikiro tsopano chakuti ndi Inu wakunena nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni anati, “Ngati tsopano mwandikomera mtima, ndionetseni chizindikiro kusonyeza kuti ndinudi mukuyankhula ndi ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa iye, Ngati mundikomera mtima mundionetse cizindikilo tsopano cakuti ndi Inu wakunena nane.