Judges 6:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mngelo wa Mulunguyo adamuuza kuti, “Tenga nyamayi pamodzi ndi makekeŵa, uziike pathanthwepo, ndi kuthira msuzi pamwamba pake.” Gideoni adachitadi zimenezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mthenga wa Mulungu ananena naye, Tenga nyamayi ndi mikate yopanda chotupitsa ndi kuziika pathanthwe pano ndi kutsanula msuzi. Ndipo anatero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mngelo wa Mulungu anamuwuza iye kuti, “Tenga nyamayi pamodzi ndi makekewa, uziyike pa mwala uwu ndi kuthirapo msuziwu.” Ndipo Gideoni anatero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mthenga wa Mulungu ananena naye, Tenga nyamayi ndi mikate yopanda cotupitsa ndi kuziika pathanthwe pano ndi kutsanula msuzi. Ndipo anatero.