Judges 6:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usiku umenewo Chauta adauza Gideoni kuti, “Utenge ng'ombe yamphongo ya bambo wako, ng'ombe ina yachiŵiri, ya zaka zisanu ndi ziŵiri, ndipo ugwetse guwa la Baala limene bambo wako ali nalo, ndi kugwetsanso fano la Asera limene lili pambali pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, usiku womwe uja Yehova ananena naye, Tenga ng'ombe ya atate wako, ndiyo ng'ombe yachiwiri ya zaka zisanu ndi ziwiri, nugamule guwa la nsembe la Baala ndilo la atate wako, nulikhe chifanizo chili pomwepo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usiku womwewo Yehova anati kwa Gideoni, “Tenga ngʼombe ya mphongo ya abambo ako, ngʼombe ina yachiwiri ya zaka zisanu ndi ziwiri ndipo ugwetse guwa la Baala limene abambo ako ali nalo, ndi kugwetsanso fano la Asera limene lili pafupi pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, usiku womwe uja Yehova ananena naye, Tenga ng'ombe ya atate wako, ndiyo ng'ombe yaciwiri ya zaka zisanu ndi ziwiri, nugamule guwa la nsembe la Baala ndilo la atate wako, nulikhe cifanizo ciri pomwepo;