Judges 6:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake pa tsiku limenelo Gideoni adatchedwa Yerubaala, ndiye kuti, “Baala alimbane naye,” poti adaagwetsa guwa lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anamutcha tsiku lija Yerubaala, ndi kuti, Amnenere mlandu Baala popeza anamgamulira guwa lake la nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho tsiku limenelo Gideoni anatchedwa, Yeru-Baala, kutanthauza kuti, “Baala alimbana naye, popeza anagwetsa guwa lake la nsembe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anamucha tsiku lija Yerubaala, ndi kuti, Amnenece mlandu Baala popeza anamgamulira guwa lace la nsembe.