Judges 6:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni adalankhula ndi Mulungu nati, “Ngati mukuti mupulumutse Aisraele ndi dzanja langa, monga momwe mwaneneramu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Gideoni anati kwa Mulungu, Mukadzapulumutsa Israele ndi dzanja langa monga mwanena,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni anati kwa Mulungu, “Ngati mudzapulumutsa Israeli ndi dzanja langa monga mwalonjezeramu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Gideoni anati kwa Mulungu, Mukadzapulumutsa Israyeli ndi dzanjalanga monga mwanena,