Judges 6:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo zidachitikadi choncho. Pamene adadzuka m'mamaŵa ndi kuufinya ubweya uja, adafinya madzi odzaza mkhate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunatero; pakuti anauka mamawa, nafinya chikopacho, nakamula mame a pachikopa, madzi ake odzala mbale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo zimenezi zinachitikadi. Gideoni atadzuka mʼmamawa ndi kuwufinya ubweya uja, anafinya madzi odzaza mtsuko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunatero; pakuti anauka mamawa, nafinya cikopaco, nakamula mame a pacikopa, madzi ace odzala mbale.