Judges 6:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidakupulumutsani kwa Aejipito ndiponso kwa onse amene ankakuzunzani. Ndidakupirikitsirani adani anu inu mulikufika, ndi kukupatsani dziko lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndinakulanditsani m'dzanja la Aejipito, ndi m'dzanja la onse akupsinja inu, ndi kuwaingitsa pamaso panu, ndi kukupatsani dziko lao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinakupulumutsani ku ulamuliro wa Igupto komanso mʼmanja mwa amene amakuzunzani. Ndinawathamangitsa adani anu inu mukufika, ndikukupatsani dziko lawo.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndinakulanditsani m'dzanja la Aaigupto, ndi m'dzanja la onse akupsinja inu, ndi kuwaingitsa pamaso panu, ndi kukupatsani dziko lao;