Judges 7:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ngati ukuwopa, uyambe wapita kuzithandoko pamodzi ndi Puri mtumiki wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati uopa kutsika, utsike naye Pura mnyamata wako kumisasa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ukuopa, upite ku msasako ndi Pura wantchito wako,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati uopa kutsika, utsike naye Pura mnyamata wako kumisasa;