Judges 7:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzamva zimene akulankhula, kenaka udzalimba mtima ndipo udzapita kukazithira nkhondo zithandozo.” Pomwepo Gideoni, pamodzi ndi Puri mtumiki wake, adapita ku mbali ina ya zithandozo, kumene kunali ankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nudzamva zonena iwo; utatero manja ako adzalimbikitsidwa kutsikira kumisasa. Pamenepo anatsikira ndi Pura mnyamata wake ku chilekezero cha anthu azida a m'misasa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ukamvere zimene akunena ndipo pambuyo pake udzalimba mtima ndi kupita kukayithira nkhondo misasayo.” Choncho iye ndi wantchito wake Pura anapita kumbali ina ya msasawo kumene kunali ankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nudzamva zonena iwo; utatero manja ako adzalimbikitsidwa kutsikira kumisasa. Pamenepo anatsikira ndi Pura mnyamata wace ku cilekezero ca anthu azidaa m'misasa.