Judges 7:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono chiŵerengero cha anthu amene adakhathira madzi pakumwa ndi manja chinali anthu 300. Koma anthu ena onse otsala adagwada pansi kuti amwe madzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kuwerenga kwa iwo akukhatira, ndi kuika dzanja lao kukamwa kwao, ndiko mazana atatu; koma ena onse anagwada pakumwa madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu 300 anamwa mokhathira, pamene ena onse anagwada pansi pakumwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi kuwerenga kwa iwo akukhatira, ndi kuika dzanja lao kukamwa kwao, ndiko mazana atatu; koma ena onse anagwada pakumwa madzi.