Judges 7:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usiku womwewo Chauta adauza Gideoni kuti, “Dzuka, pita ukazithire nkhondo zithandozo, pakuti ndazipereka m'manja mwako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali usiku womwewo, kuti Yehova ananena naye, Tauka, tatsikira kumisasa; pakuti ndaipereka m'dzanja lako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usiku umenewo Yehova anati kwa Gideoni, “Dzuka, pita kachite nkhondo ku misasayo, chifukwa ndayipereka mʼmanja mwako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali usiku womwewo, kuti Yehova ananena naye, Tauka, tatsikira kumisasa; pakuti ndaipereka m'dzanja lako.