Judges 8:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Gideoni mwana wa Yoasi adabwerako ku nkhondo kudzera ku chikweza cha Heresi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Gideoni mwana wa Yowasi anabwerera kunkhondo pokwerera pa Heresi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Gideoni mwana wa Yowasi, pobwera kuchokera ku nkhondo anadzera njira ya ku chikweza cha Heresi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Gideoni mwana wa Yoasi anabwerera kunkhondo pokwerera pa Heresi.