Judges 8:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Gideoni adagwira akuluakulu amumzindamo, ndipo adatenga matsatsa a minga yam'chipululu, naŵakwapula anthu a ku Sukotiwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anagwira akulu a m'mudzi ndi minga ya kuchipululu ndi mitungwi, nawalanga nazo amuna a ku Sukoti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Gideoni anatenga akuluakulu a mu mzindawo ndipo anagwira matsatsa a minga za mʼchipululu ndi kuwakwapula nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anagwira akulu, a m'mudzi ndi minga ya kucipululu ndi mitungwi, nawalanga nazo amuna a ku Sukoti.