Judges 8:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adagwetsa nsanja ya ku Penuwele ija, napha anthu onse amumzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anagamula nsanja ya Penuwele, napha amuna akumudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anagwetsa nsanja ya ku Penueli ndi kupha amuna onse a mu mzindawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anagamula nsanja ya Penueli, napha amuna a kumudzi.