Judges 8:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni adaŵauza kuti, “Amene aja anali abale anga, ana a mai wanga. Ndikulumbira pamaso pa Chauta kuti, ‘Mukadapanda kuŵapha, inenso sindikadakuphani.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati, Ndiwo abale anga, ana a mai wanga. Pali Yehova mukadawasunga amoyo, sindikadakuphani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Gideoni anayankha kuti, “Ndikulumbira pa Mulungu, mukanapanda kuwapha nanenso sindikanakuphani. Ndi abale anga amenewo, ana a amayi anga enieni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati, Ndiwo abale anga, ana a mai wanga. Pali Yehova mukadawasunga amoyo, sindikadakuphani.