Judges 8:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adaŵayankha kuti, “Ndachita chiyani ine kuyerekeza ndi zimene mwachita inu? Kodi zimene mwachita inu Aefuremu si zazikulu koposa zimene fuko langa la Abiyezere lachita?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ananena nao, Ndachitanji tsopano monga inu? Kodi kukunkha mphesa kwa Efuremu sikuposa kutchera mphesa kwa Abiyezere?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iye anawayankha kuti, “Nʼchiyani ndachita kuyerekeza ndi zimene mwachita inu? Kodi zimene mwachita inu Aefereimu si zazikulu kuposa zimene fuko langa la Abiezeri lachita?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ananena nao, Ndacitanji tsopano monga inu? Kodi kukunkha mphesa kwa Efraimu sikuposa kuchera mphesa kwa Abiezeri?