Judges 8:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Aisraele adamuuza Gideoni kuti, “Muzitilamulira inuyo, mwana wanu ndi zidzukulu zanu, pakuti ndinu amene mwatipulumutsa kwa Amidiyani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anthu a Israele anati kwa Gideoni, Mutilamulire ndi inu, ndi mwana wanu, ndi mdzukulu wanu, pakuti mwatipulumutsa m'dzanja la Amidiyani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli anati kwa Gideoni, “Inu muzitilamulira, mwana wanu ndi zidzukulu zanu, chifukwa mwatipulumutsa mʼmanja mwa Amidiyani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anthu a Israyeli anati kwa Gideoni, Mutilamulire ndi inu, ndi mwana wanu, ndi mdzukulu wanu, pakuti mwatipulumutsa m'dzanja la Amidyani.