Judges 8:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Gideoni adaŵayankha kuti, “Ine sindidzakulamulirani, mwana wanganso sadzakulamulirani. Chauta ndiye amene adzakulamulirani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Gideoni ananena nao. Sindidzalamulira inu, ngakhale mwana wanga sadzalamulira inu; Yehova adzalamulira inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Gideoni anawawuza kuti, “Sindidzakulamulirani, mwana wanganso sadzakulamulirani. Koma Yehova ndiye adzakulamulirani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Gideoni ananena nao. Sindidzalamulira inu, ngakhale mwana wanga sadzalamulira inu; Yehova adzalamulira inu.