Judges 8:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni adaŵauzanso kuti, “Ndikupempheni kanthu kamodzi. Aliyense mwa inu andipatse ndolo zimene adafunkha.” (Adani aja anali ndi ndolo zagolide chifukwa chakuti anali Aismaele).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gideoni anatinso kwa iwo, Mundilole ndipemphe kanthu kamodzi kwa inu, mundipatse aliyense maperere mwa zofunkha zanu; pakuti anali nao maperere agolide, pokhala anali Aismaele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni anatinso, “Ine ndikupemphani chinthu chimodzi. Aliyense wa inu andipatse ndolo zomwe anafunkha ku nkhondo.” (Adani aja anali ndi ndolo zagolide popeza anali Aismaeli).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gideoni anatinso kwa iwo, Mundilole ndipemphe kanthu kamodzi kwa inu, mundipatse ali yense mapelele mwa zofunkha zanu; pakuti anali nao mapelele agolidi, pokhala anali Aismayeli.