Judges 8:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni mwana wa Yoasi adapita kukakhala kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yerubaala, mwana wa Yowasi anamuka, nakhala m'nyumba ya iye yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yeru-Baala mwana wa Yowasi anapita kukakhala kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yerubaala, mwana wa Yoasi anamuka, nakhala, m'nyumba ya iye yekha.