Judges 8:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anali nawo ana 70, akeake ndithu, pakuti anali ndi akazi ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakhala nao ana amuna makumi asanu ndi awiri Gideoni, anawabala ndi iye; popeza anali nao akazi ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Gideoni anali 70 popeza anali ndi akazi ambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakhala nao ana amuna makumi asanu ndi awiri Gideoni, anawabala ndi iye; popeza anali nao akazi ambiri.