Judges 8:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzikazi wake wina amene anali ku Sekemu, adamubaliranso mwana dzina lake Abimeleki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mkazi wake wamng'ono wokhala m'Sekemu, iyenso anambalira mwana wamwamuna; namutcha dzina lake Abimeleki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mdzakazi wake amene anali ku Sekemu, anabereka naye mwana wamwamuna, amene anamutcha Abimeleki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mkazi wace wamng'ono wokhala m'Sekemu, iyenso anambalira mwana wamwamuna; namucha dzina lace Abimeleki.