Judges 8:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gideoni, mwana wa Yoasi, adafa ndi ukalamba, naikidwa m'manda a Yoasi bambo wake ku Ofura, mzinda wa Abiyezere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Gideoni mwana wa Yowasi anafa atakalamba bwino, naikidwa m'manda a Yowasi atate wake, m'Ofura wa Aabiyezere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gideoni mwana wa Yowasi anamwalira atakalamba ndipo anayikidwa mʼmanda a abambo ake, Yowasi ku Ofura mzinda wa Mwabiezeri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Gideoni mwana wa Yoasi anafa atakalamba bwino, naikidwa m'manda a Yoasi atate wace, m'Ofira wa Aabiezeri.