Judges 8:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atangomwalira Gideoni, Aisraele adayambanso kupembedza Abaala, nasandutsa Baala wa Chipangano mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atafa Gideoni, ana a Israele anabwereranso nagwadira Abaala, nayesa Baala-Beriti mulungu wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atangomwalira Gideoni, Aisraeli anayambanso kupembedza Abaala. Iwo anasandutsa Baala-Beriti kukhala mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atafa Gideoni, ana a Israyeli anabwereranso nagwadira Abaala, nayesa Baala-beriti mulungu wao.