Judges 8:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraelewo sadakumbukirenso Chauta, Mulungu wao, amene adaŵapulumutsa kwa adani ao onse a mbali ndi mbali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana a Israele sanakumbukire Yehova Mulungu wao, amene anawapulumutsa m'dzanja la adani ao onse pozungulira ponse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli sanakumbukirenso Yehova Mulungu wawo amene anawapulumutsa mʼmanja mwa adani awo mbali zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana a Israyeli sanakumbukila Yehova Mulungu wao, amene anawapulumutsa m'dzanja la adani ao onse pozungulira ponse;